A Malawi ambiri adabwa ndi mkhalidwe wa a mtsogoleri wa kale wa dziko lino a Peter Mutharika omwe adanyamula sofa nkukakhalapo kumanda nthawi yamaliro.

Izi zikutsutsana ndi kapena kuti zikusemphana ndi chikhalidwe cha chimalawi.

Anthu ambiri ayankhulapo ndipo adzudzula a Mutharika powanena kuti zomwe apangazo zikusemphana ndi chikhalidwe cha Chimalawi.

Ku Malawi timalemekeza kwambiri maliro ndipo timaitcha kuti mfumu. Tikunena pano, anthu akugawana zithunzi pa masamba a michezo ndinso pa internent.

 

 

 

 

One thought on “A Mutharika adabwitsa a Malawi pokhala pampando wa chifumu ku manda”

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *