Mtsogoleri wadziko lino a Dr Lazarus McCarthy Chakwera afika m’zinda wa Maputo m’dziko la Mozambique komwe mwazina iwo akuyembekezeka kukhala ndi zokambirana ndi mtsogoleri wa Dzikolo a Filipe Nyusi kunyumba yaboma kumeneko. Ali ku Mozambique , Chakwera akuyembekezeka kusainilana mgwirizano okhudza nkhani za malonda. Malingana ndi chikalata chomwe tapeza , ulendo umenewu uthandizaso kupititsa patsogolo ntchito yogula 41 megawatts. During the trip the two countries are expected to strengthening the 41 megawatts power interconnection project as well as normalizing the transportation of petroleum products. The talks also borders on improving the movement of people and goods to boost trade as refurbishing the Nacala railway line. Zokambirana zikhudzanso kayendedwe ka anthu am’maiko amenewa. Ali Ku Mozambique , Chakwera akuyembekezeka kumpatsa ulemu wa padela wakayendetsedwe ka ntchito za kunja kuchokera ku Joaquim Chissano University. Post navigation Chakwera arrives safely in Mozambique for bilateral talks with Nyusi NCIC whips Steal Malata, closes its construction site