Mkhalakale pandale a Uladi Mussa omwe alowa chipani cha Malawi Congress (MCP) lero ku Salialonjeza kuti agwira ntchito ndi mtima wawo onse pofuna kuonetsetsa kuti Mtsogoleri wa dziko lino adzapambane mosabvuta pa masankho a 2025. A Mussa adadzudzula chipani cha Democratic Progressive (DPP) kamba kowaimika minyezi khumi ndi inawi ngati kuti ndi mzimai oyembekezera. A Uladi Mussa alonjeza kuthandiza Chakwera A Mussa adaseketsa wanthu pomwe iwo anafusa ngati iwo ndi oyembekezera. A Mussa adati iwo ndi amene adagwira ntchito kuti a Bingu wa Mutharika awine ma ulendo onse awiri komanso ndi amene adathandiza a Bakili Muluzi ndinso a Peter Mutharika. Post navigation Karonga Youth Activist, Simsokwe becomes “political scammer” Chakwera officially receives 66 new Secondary Schools from USA Government