Patangotha nthawi pang’ono Mkulu wa bungwe lija la Human Rights Defendance Coalition (HRDC) Gift Trapence, atayamikila Ndondomeko ya zachuma yachaka chino, naye mkhala kale wina pa nkhani za ulamuliro wabwino a Undule Mwakasungula abwera poyera kuyamikila boma ka ndondomeko ya zachuma ya chaka chino ndi kumayambiriro kwa chaka cha mawa. A Mwakasungula ati ndondomeko imeneyi ili ndi kuthekela kwa kusintha zinthu mdziko muno. Iwo anapempha boma kuti liyendetse ntchito za chumazi molingangana ndi ndondomeko imeneyi. Undule Mwakasungula: Akuti ndondomeko ya iyi ili bwino Post navigation Governance expert Undule Mwakasungula weighs in on budget Air Cargo donates equipment to Chileka Health Centre