M’neneli wa ku Nyumba ya Boma a Anthony Kasunda ayankhulapo pa malipoti omwe  newspapera ina mdziko muno yafalitsa kuti ndalama zomwe nyumba yaboma imapereka kwa ogwira ntchito zakwera modetsa nkhawa.

A Kasunda atsutsa za malipoti amenewo.

Anthony Kasunda

Malinga ndi kalata yomwe wasainila ndi ofalitsa nkhaniyu, malipotiwa ndi khamba kamwa chabe ndipo kuti pakadali pano nyuzipepalayi yapatsidwa uthenga oyenelela molingana ndi khaniyi pofuna kuonetsetsa kuti anthu akupatsidwa uthenga oyenelela molingana ndi ndondomeko ya chuma ya chaka chino.

Kalatayi yapitiliza kunena kuti mtsogoleli wa dziko lino Dr. Lazarus Chakwera ndi khumbo lake kufuna kupeleka uthenga oyenelela ku nyumba zoulutsa mawu mdziko muno.

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *