Mkhalakale pandale a Uladi Mussa omwe alowa chipani cha Malawi Congress (MCP) lero ku Salialonjeza kuti agwira ntchito ndi mtima wawo onse pofuna kuonetsetsa kuti Mtsogoleri wa dziko lino adzapambane mosabvuta pa masankho a 2025.

A Mussa adadzudzula chipani cha Democratic Progressive (DPP) kamba kowaimika minyezi khumi ndi inawi ngati kuti ndi mzimai oyembekezera.

A Uladi Mussa alonjeza kuthandiza Chakwera

A Mussa adaseketsa wanthu pomwe iwo anafusa ngati iwo ndi oyembekezera.

A Mussa adati iwo ndi amene adagwira ntchito kuti a Bingu wa Mutharika awine ma ulendo onse awiri komanso ndi amene adathandiza a Bakili Muluzi ndinso a Peter Mutharika.

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *