Patangotha nthawi pang’ono Mkulu wa bungwe lija la Human Rights Defendance Coalition (HRDC) Gift Trapence, atayamikila Ndondomeko ya zachuma yachaka chino, naye mkhala kale wina pa nkhani za ulamuliro wabwino a Undule Mwakasungula abwera poyera kuyamikila boma ka ndondomeko ya zachuma ya chaka chino ndi kumayambiriro kwa chaka cha mawa.

A Mwakasungula ati ndondomeko imeneyi ili ndi kuthekela kwa kusintha zinthu mdziko muno.

Iwo anapempha boma kuti liyendetse ntchito za chumazi molingangana ndi ndondomeko imeneyi.

 

 

Undule Mwakasungula: Akuti ndondomeko ya iyi ili bwino

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *