Polankhula mumzinda wa Blantyre , a Lazarus Chakwera ati , Chipatala chomwe amanga a Dr Thom Mpinganjira chithandiza kwambiri patchito yotukula ntchito za umoyo mdziko muno.

A Chakwera ati boma limaononga ndalama zokwana $15,000 pamunthu mmodzi kuti apite akalandire nthandizo kunja.

A Chakwera anaonjezera kuti zateromu boma lasiya kuononga ndalama chifukwa pakadali pano zipatala zonga izi zilinso ku Lilongwe.

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *