Phungu wa chigawo cha pakati mu mzinda wa Lilongwe , Alfred Jiya lero adatsagana ndi nduna ya madzi Abida Mia kumwambo okalandila chitukuko cha madzi chomwe kampani ya Sun Gold yamanga mdelari. Mukulankhula kwake a Jiya adayamikila kampaniyi kamba ka ntchito yobweretsa madzi awukhondo mudelari. Jiya -Abida Mia kulandila chitukuko cha Madzi Mmawu ake Nduna yoona za Madzi Abida Mia adayamikila kampane ya Sun Gold komanso Paramount Holdings kamba kopereka madzi mwa ulere kwa anthu okhala mumzinda wa Lilongwe uku ndi kwa Mgona . Post navigation LWB making strides in conserving tree cover We Lose Kaning’ina Forest, we are Doomed – NRWB