Mkulu wa World Bank kuno ku Malawi a Hugh Ridell wati ndiwokhutira ndimene boma la Malawi pansi pa utsogoleri wa Dr Lazarus chakwera likugwilira ntchito zake polimbikitsa maphuziro mdziko muno. Iwo anena izi pa mwambo womwe ukuchitikira ku Dedza komwe mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus chakwera watsegulira ntchito yomanga zipinda zophunzilira. Dr Lazarus McCarthy Chakwera in Dedza Pali chiyembekezo chakuti ophunzira okwana 1 Million ndiwo apindule kuchokera ku ntchito yomanga zipinda zophunzilira zokwana 10,900. Post navigation Chakwera commends Speaker of Parliament for professional conduct Governance expert Undule Mwakasungula weighs in on budget