Polankhula mumzinda wa Blantyre , a Lazarus Chakwera ati , Chipatala chomwe amanga a Dr Thom Mpinganjira chithandiza kwambiri patchito yotukula ntchito za umoyo mdziko muno. A Chakwera ati boma limaononga ndalama zokwana $15,000 pamunthu mmodzi kuti apite akalandire nthandizo kunja. A Chakwera anaonjezera kuti zateromu boma lasiya kuononga ndalama chifukwa pakadali pano zipatala zonga izi zilinso ku Lilongwe. Post navigation Enact Termination of Pregnancy Bill to save women’s lives, – CSOs How Malawi is fighting infant mortality through MCG initiative in Ntchisi