Kudali chimwemwe ndinso chisangalaro m’boma la Karonga pamene mtsogoleri wadziko lino a Lazarus Chakwera adakachereza anthu omwe adakhudzidwa ndi amadzi osefukira mu m’bomalo.

Wena sadakhulupilire koma zachitikadi kuona mtsogoleri wadziko kuyenda mtunda wautali wapansi kuchereza anthu omwe adakhudzidwa ndi madzi osefukira amewo.

A Chakwera ku Karonga

Mukuyankhula kwawo mbomali, a Chakwera analimbikitsitsa anthu mbomalo kuti boma lawo lipereka chisamaliro chokwanila kwa a Malawi okhudzidwawo.

Chakwera adapereka katundu osiyana siyana kwa anthu okhudzidwa.

 

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *