National Malawi akupitilira kuchita bwino pankhani za ma ufulu osiyana siyana December 28, 2023 Apereka ndondomeko ya ma ufulu ku Dakar Senegal Malawi ndi dziko limodzi lomwe mbiri yake ili bwino kwambiri pankhani dzokhuza ma ufulu osiya na siyana. Izi zadza kamba koti mtsogoleri…
Water and Sanitation Kampani ya Windmill Africa ipempha a Malawi kuti ayambe kugwiritsa ntchito zipangizo zoyendera mphepo December 27, 2023 A Malawi awalangiza kuti ayike chidwi chawo pa nkhani ya ulimi othilira pogwirita ntchito zipangizo za luso loyendela mphepo. Mkulu wa Kampani ya Africa Windmill a Gibozi Mphanzi ndi amene…
National Chipasupasu chabuka mchipani cha DPP pa nkhani ya oyenela kuponya vote ku msonkhano wa ukulu wa convention December 27, 2023 A Namalomba kuyankhula kwa atolankhani Kusamvana kwabuka mchipani cha Democratic Progressive (DPP), pamene yemwe ali mkulu otsutsa kunyumba ya Malamulo a Kondwani Nankhumwa atemetsa nkhwangwa pa mwala kukana kuti iwo…
Business Boma lilibe maganizo opanga K10,000 yogwirana watero Mkulu wa Banki yaikulu ya Reserve a Dr Wilson Banda December 27, 2023 Mkulu wa Banki yaikulu ya m’dzimo muno ya Reserve Dr Wilson Banda watsutsa phekesera zomwe zikumveka maka pa masamba a michezo zomwe a Malawi ambiri akugawana kuti Boma lili ndi…
National A Malawi chuluka akupitilirabe kulandila chimanga chochuluka mdziko muno December 27, 2023 Mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus McCarthy Chakwera akupitiliza ntchito yogawa chimanga kwa a Malawi omwe akukhudzidwa ndi njala. Izi zikugwirizana ndi mawu omwe a Chakwera adanena m’nyumba ya Malamulo…
Business Castel Malawi brings Spirits of Malawi festive editions December 27, 2023 Giant alcoholic beverages producer Castel Malawi has unveiled the Special Christmas Limited Edition of the ‘Spirits of Malawi’ with special Christmas labels and packaging for new customer experience. Castel Malawi…
Business PCL cheers the elderly with Christmas gifts in Mpemba December 27, 2023 Conglomerate Press Corporation plc (PCL) on Friday gave an early Christmas gift to the elderly in Mpemba, Blantyre by donating food packs and treating them to a Christmas luncheon. Speaking…
Politics Nankhumwa warns DPP against tampering with voting electoral college December 26, 2023 Hon Kondwani Nankhumwa addressing the press The leader of opposition in Parliament Kondwani Nankhumwa has warned Democratic Progressive Party (DPP) Madala team against tampering with the electoral college as being…
National Malawi Police announces reduced cases of albino attacks December 26, 2023 President Dr Lazarus McCarthy Chakwera with people living with albinism Malawi Police Services has announced that the cases of attacking people with albinism have drastically reduced compared with similar cases…
Business Nduna ya za mtengatenga a Jacob Hara idandaula kamba ka kuchedwa kwa ntchito ya nseu wa magawo asanu ndi limodzi (Six Lane) December 26, 2023 Olemekeza a Jacob Hara at ndi okhumudwa ndi ntchito yomanga mseu wa magawo asanu ndi imodzi Nduna yoona ntchito za mtengatenga ndi mtokoma a Jacob Hara apempha kampani ya ku…