Business Sports NBM Plc impressed with Scorchers’ winning start to Olympic qualifiers October 13, 2026
Business CEAR announces full resumption of Railway transport system to Lilongwe May 24, 2024 Central and Eastern African Railway Company has officially announced full resumption of its railway connectivity drive which the company has been working on from Blantyre to Lilongwe. Economists view the…
Business Bungwe la MCCCI limtaira kamtengo Chakwera pankhani ya dongosolo la dzachuma May 24, 2024 Mkulu wa bungwe loona za malonda la Confederation of Chambers of Commerce and Industry (MCCCI) a Dr Wisely Phiri ayamikira Mtsogoleri wa dziko lino a Dr Dr Lazarus McCarthy Chakwera…
Business Mlendo olemekezeka kwambiri nduna yaikulu ya dziko la Iceland a Bjarni Benediktsson abwerera kumudzi kwawo May 24, 2024 Nduna yaikulu ya dziko la Iceland a Bjarni Benediktsson abwerera kumudzi kwawo ku Iceland dzulo atamaliza ulendo wawo wa masiku asanu. A Benediktsson adafika mdziko muno pa 19 May, 2024,…
Business Chakwera waulura njira zammene Chuma cha dziko lino chingapitire patsogolo May 24, 2024 Tate fuko la Malawi Dr Lazarus McCarthy Chakwera wabwera poyera kulangiza a Malawi njira zomwe akuyenera kutsata ndi cholinga cholinga chokweza chuma cha dziko lino. Mukulankhula kwawo ku Blantyre pamwambo…
Business Chakwera for more exports May 24, 2024 By Kondanani Chilimunthaka President Lazarus Chakwera has urged the Malawian business community to strive for more production that will be exported to other countries for economic growth of Malawi. He…
Business Chakwera atsegulira chionetsero chazamalonda komwe wapempha a Malawi kuti apewe kuitanitsa chilihonse kunja May 23, 2024 Mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera lero watsekulira chionetsero chazamalonda mum’zinda wa Blantyre. Mukulankhula kwawo a Chakwera, adayamikira bungwe la Malawi Confederation of Chambers of Commerce and Industry (MCCCI)…
Business Iceland Government pledges additional support for Malawi May 23, 2024 Iceland Prime Minister Bjarni Benediktsson, on Thursday concluded his five day state visit to Malawi with commitment to further strengthen bilateral relationship with Malawi. Speaking a press conference at Kamuzu…
Politics MCP iyankha azibusa pa nkhani ya msonkhano waukulu wa convention May 22, 2024 Chipani cha Malawi Congress (MCP) chalembera kalata azibusa achinyamata omwe amadzitcha young Pastors Network (YPN). Azibusawa kummawaku anadzudzula chipani cha MCP ati kamba ka dongosolo lomwe chipanichi chidatutsa posachedwapa zomwe…
Business Matours Bus Service safety under microscope May 22, 2024 Malawi has registered a boom of bus lines following the liquidation of Shire bus services formerly known as UTM which enjoyed the monopoly of the transport business in those days.…
Business Chakwera on point: Malawians should reject Mutharika’s deceptions May 22, 2024 BIRD’S VIEW EYE- COLUMN – MALAWI EXCLUSIVE President Dr Lazarus Chakwera recently delivered a poignant truth with eloquence and precision: the agony that Malawians endure today is the bitter fruit…